Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno khoma la mzindawo linabooledwa,+ ndipo amuna onse ankhondo anathawa usiku kudzera pachipata chimene chinali pakati pa makoma awiri, pafupi ndi munda wa mfumu.+ Akasidi+ anali atazungulira mzinda wonsewo, ndipo mfumuyo inayamba kuthawa+ kulowera cha ku Araba.+

  • Yeremiya 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo ndidzatenga zinthu zonse zosungidwa mumzindawu, katundu wawo yense, zinthu zonse zamtengo wapatali ndi chuma chonse cha mafumu a Yuda, n’kuzipereka m’manja mwa adani awo.+ Ndipo adaniwo adzafunkha zinthu zimenezi ndi kupita nazo ku Babulo.+

  • Yeremiya 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu, ine ndichititsa zida zimene zili m’manja mwanu kukutembenukirani. Zimenezi ndi zida zimene mukugwiritsa ntchito pomenyana ndi mfumu ya Babulo+ ndi Akasidi+ amene azungulira kunja kwa mpanda wanu. Ndipo ndisonkhanitsa zida zanuzo pakati pa mzinda uwu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena