Deuteronomo 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+ Salimo 115:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzadalitsa anthu omuopa,+Adzadalitsa onsewo osasiyapo aliyense.+
29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+