Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.

  • Ekisodo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova ndi wankhondo.+ Dzina lake ndi Yehova.+

  • Yeremiya 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+

  • Amosi 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova ndilo dzina+ la amene anapanga gulu la nyenyezi la Kima+ ndi gulu la nyenyezi la Kesili,+ amene amachititsa mdima wandiweyani+ kukhala kuwala kwa m’mamawa, amenenso amachititsa masana kukhala mdima ngati wausiku,+ amene amaitana madzi akunyanja kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.+

  • Amosi 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Yehova ndilo dzina+ la amene amamanga makwerero ake kumwamba+ ndi kumanganso nyumba pamwamba pa dziko lapansi limene analikhazikitsa,+ amene amaitana madzi akunyanja+ kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena