Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Motero Mulungu anapanga zounikira zikuluzikulu ziwiri. Chounikira chokulirapo anachipanga kuti chilamulire usana, ndi chocheperapo kuti chilamulire usiku, komanso nyenyezi.+

  • Salimo 89:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Udzakhazikika ngati mwezi mpaka kalekale,

      Udzakhala ngati mboni yokhulupirika ya m’mlengalengayo.” [Seʹlah.]

  • Yesaya 54:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+

  • Yeremiya 31:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Yehova ndiye Wopereka dzuwa kuti liziwala masana,+ woikira mwezi malamulo,+ wopereka nyenyezi+ kuti ziziwala usiku,+ amene amavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Wochita zimenezi dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye wanena kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena