Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ Deuteronomo 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola kumeneko.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti uzichita zimenezi.
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
18 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola kumeneko.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti uzichita zimenezi.