Machitidwe 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Popeza panali patapita kale nthawi yaitali, ndipo kuyenda panyanja tsopano kunali koopsa chifukwa ngakhale nthawi ya kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba machimo+ inali itadutsa kale, Paulo anawapatsa malangizo.
9 Popeza panali patapita kale nthawi yaitali, ndipo kuyenda panyanja tsopano kunali koopsa chifukwa ngakhale nthawi ya kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba machimo+ inali itadutsa kale, Paulo anawapatsa malangizo.