Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Aneneriwo anali kukuuzani kuti, ‘Chonde, aliyense wa inu atembenuke ndi kusiya njira yake yoipa ndi zochita zake zoipa+ kuti mupitirize kukhala m’dziko limene Yehova anakupatsani, inuyo ndi makolo anu. Anakupatsani dzikoli kuti chikhale cholowa chanu kwa nthawi yaitali.+

  • Yona 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Munthu aliyense komanso ziweto zivale chiguduli. Afuulire Mulungu ndi mphamvu zawo zonse, ndipo aliyense asiye njira zake zoipa+ ndi zinthu zonse zachiwawa zimene amachita.

  • Zekariya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Musakhale ngati makolo anu+ amene aneneri akale anawauza mofuula+ kuti: “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chonde, siyani njira zanu zoipa ndi zochita zanu zoipa n’kubwerera kwa ine!’”’+

      “‘Koma iwo sanamvere ndipo sanalabadire mawu anga,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena