Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+ Yeremiya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto+ kuti: “‘Yehova wanena kuti: “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyang’anani mokwiya anthu inu+ pakuti ndine wokhulupirika,”+ watero Yehova.+ “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+ Hoseya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Iwe Isiraeli, bwerera kwa Yehova Mulungu wako+ pakuti wapunthwa mu zolakwa zako.+
12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto+ kuti: “‘Yehova wanena kuti: “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyang’anani mokwiya anthu inu+ pakuti ndine wokhulupirika,”+ watero Yehova.+ “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+