Yeremiya 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Akalongawo anasiya mpukutuwo m’chipinda chodyera+ cha Elisama+ mlembi. Kenako analowa m’bwalo+ kuti akaonane ndi mfumu, ndipo anayamba kuuza mfumu nkhani yonse yokhudza mpukutuwo.
20 Akalongawo anasiya mpukutuwo m’chipinda chodyera+ cha Elisama+ mlembi. Kenako analowa m’bwalo+ kuti akaonane ndi mfumu, ndipo anayamba kuuza mfumu nkhani yonse yokhudza mpukutuwo.