2 Mbiri 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Pali buku+ limene wansembe Hilikiya wandipatsa.”+ Ndiyeno Safani anayamba kuwerenga bukulo pamaso pa mfumu.+
18 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Pali buku+ limene wansembe Hilikiya wandipatsa.”+ Ndiyeno Safani anayamba kuwerenga bukulo pamaso pa mfumu.+