2 Mafumu 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya. 1 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya,+ ndipo wachinayi anali Salumu.
18 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina, ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.
15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya,+ ndipo wachinayi anali Salumu.