Genesis 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atatero, anamutenga n’kukamuponya m’chitsimecho.+ Pa nthawiyo chitsimecho chinali chopanda madzi. Salimo 109:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikawachitira zabwino amandibwezera zoipa,+Ndikawasonyeza chikondi amandibwezera chidani.+ Maliro 3:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Anali kufuna kuchotsa moyo wanga kuti andiponye m’dzenje+ ndipo anali kundiponya miyala.