Yeremiya 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+ Yeremiya 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+
20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+
6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+