Yeremiya 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika pa Chipata cha Benjamini,+ anakumana ndi mkulu wa alonda amene dzina lake linali Iriya mwana wa Selemiya, mwana wa Hananiya. Nthawi yomweyo Iriya anagwira mneneri Yeremiya ndi kunena kuti: “Ukuthawira kwa Akasidi!”
13 Atafika pa Chipata cha Benjamini,+ anakumana ndi mkulu wa alonda amene dzina lake linali Iriya mwana wa Selemiya, mwana wa Hananiya. Nthawi yomweyo Iriya anagwira mneneri Yeremiya ndi kunena kuti: “Ukuthawira kwa Akasidi!”