Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo.

  • Yeremiya 40:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma Yeremiya anali asanaganize zobwerera pamene Nebuzaradani anamuuza kuti: “Bwerera kwa Gedaliya,+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ amene mfumu ya Babulo yamuika kukhala wolamulira mizinda ya Yuda. Ukakhale naye pakati pa anthu ako ndipo ukapite kulikonse kumene ungakonde kupita.”+

      Pamenepo mkulu wa asilikali olondera mfumu anamupatsa chakudya chapaulendo ndi mphatso ndipo anamulola kupita.+

  • Yeremiya 41:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena