1 Mafumu 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako aliyense anayamba kupha mdani wake. Asiriyawo+ anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa. Koma Beni-hadadi mfumu ya Siriya anathawa atakwera hatchi, pamodzi ndi amuna ena okwera pamahatchi. Yobu 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kuti pa tsiku la tsoka woipa amapulumuka,+Ndipo pa tsiku la mkwiyo amawomboledwa?
20 Kenako aliyense anayamba kupha mdani wake. Asiriyawo+ anayamba kuthawa+ ndipo Aisiraeli anawathamangitsa. Koma Beni-hadadi mfumu ya Siriya anathawa atakwera hatchi, pamodzi ndi amuna ena okwera pamahatchi.