Yeremiya 42:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musachite mantha ndi mfumu ya Babulo imene mukuiopayo.’+ “‘Mfumu imeneyi musachite nayo mantha,+ chifukwa ine ndili ndi inu kuti ndikupulumutseni ndi kukulanditsani m’manja mwake,’+ watero Yehova.
11 Musachite mantha ndi mfumu ya Babulo imene mukuiopayo.’+ “‘Mfumu imeneyi musachite nayo mantha,+ chifukwa ine ndili ndi inu kuti ndikupulumutseni ndi kukulanditsani m’manja mwake,’+ watero Yehova.