1 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+ Machitidwe 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komatu sindinakubisireni chilichonse chopindulitsa, ndipo sindinaleke kukuphunzitsani+ poyera komanso kunyumba+ ndi nyumba.
18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+
20 Komatu sindinakubisireni chilichonse chopindulitsa, ndipo sindinaleke kukuphunzitsani+ poyera komanso kunyumba+ ndi nyumba.