Yeremiya 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Munthu wakufa musamulire kapena kumumvera chisoni anthu inu.+ Lirani munthu amene watengedwa kupita ku ukapolo chifukwa sadzabwererakonso ndipo sadzaonanso dziko lakwawo. Yeremiya 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndidzakuponyani kudziko limene mitima yanu idzalakalaka kubwererako, koma simudzabwererako.+
10 “Munthu wakufa musamulire kapena kumumvera chisoni anthu inu.+ Lirani munthu amene watengedwa kupita ku ukapolo chifukwa sadzabwererakonso ndipo sadzaonanso dziko lakwawo.