Danieli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+ amachotsa mafumu ndi kuika mafumu,+ amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+ Danieli 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mfumu, Mulungu Wam’mwambamwamba+ anapatsa bambo anu+ Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+
21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+ amachotsa mafumu ndi kuika mafumu,+ amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+
18 Inu mfumu, Mulungu Wam’mwambamwamba+ anapatsa bambo anu+ Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+