Numeri 16:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 zofukizira za amuna amene anafa+ chifukwa cha kuchimwa. Azisule kuti zikhale timalata topyapyala n’kukutira nato guwa lansembe,+ popeza anafika nazo pamaso pa Yehova, ndipo zakhala zopatulika. Timalatato tikhale chikumbutso kwa ana a Isiraeli.’”+ Yeremiya 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ watero Yehova.+ ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha kuti achite manyazi pankhope zawo?’+
38 zofukizira za amuna amene anafa+ chifukwa cha kuchimwa. Azisule kuti zikhale timalata topyapyala n’kukutira nato guwa lansembe,+ popeza anafika nazo pamaso pa Yehova, ndipo zakhala zopatulika. Timalatato tikhale chikumbutso kwa ana a Isiraeli.’”+
19 ‘Kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ watero Yehova.+ ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha kuti achite manyazi pankhope zawo?’+