Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.

  • Numeri 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo+ ya Aroni patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana a chipandukowa,+ n’cholinga chakuti aleke kudandaula motsutsana ndi ine, kuti angafe.”

  • Numeri 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+

  • 1 Timoteyo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena