Salimo 51:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kudzimvera chisoni mumtima ndizo nsembe zimene Mulungu amavomereza.+Inu Mulungu, simudzanyoza mtima wosweka ndi wophwanyika.+
17 Kudzimvera chisoni mumtima ndizo nsembe zimene Mulungu amavomereza.+Inu Mulungu, simudzanyoza mtima wosweka ndi wophwanyika.+