-
Numeri 30:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 mwamuna wake n’kumva koma osanenapo kanthu, osam’kaniza, malonjezo ake onse akhale momwemo, ndipo lonjezo lililonse lodzimana limene walumbirira moyo wake likhale momwemo.
-
-
Numeri 30:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ngati mwamunayo sananenepo kanthu kwa mkazi wake, masiku n’kumapita, ndiye kuti mwamunayo wakhazikitsa malonjezo onse a mkaziyo, kapena malonjezo onse odzimana amene mkaziyo walumbirira moyo wake.+ Iye wawakhazikitsa chifukwa sananenepo kanthu kwa mkaziyo pa tsiku limene anamumva akulonjeza.
-