Yeremiya 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 chifukwa cha zoipa zonse zimene ana a Isiraeli+ ndi ana a Yuda+ achita ndi kundikhumudwitsa nazo.+ Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo,+ aneneri awo,+ amuna a mu Yuda ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu. Ezekieli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimene akuluakulu a Isiraeli akuchita mu mdima?+ Kodi waona zimene aliyense wa iwo akuchita m’chipinda chamkati mmene muli fano lake losema? Iwo akunena kuti, ‘Yehova sakutiona.+ Yehova wachokamo m’dziko muno.’”
32 chifukwa cha zoipa zonse zimene ana a Isiraeli+ ndi ana a Yuda+ achita ndi kundikhumudwitsa nazo.+ Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo,+ aneneri awo,+ amuna a mu Yuda ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu.
12 Ndiyeno iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimene akuluakulu a Isiraeli akuchita mu mdima?+ Kodi waona zimene aliyense wa iwo akuchita m’chipinda chamkati mmene muli fano lake losema? Iwo akunena kuti, ‘Yehova sakutiona.+ Yehova wachokamo m’dziko muno.’”