Yobu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mu mdima iye amathyola nyumba za anthu,Masana iwo amadzitsekera m’nyumba,Ndipo saona kuwala kwa masana.+ Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
16 Mu mdima iye amathyola nyumba za anthu,Masana iwo amadzitsekera m’nyumba,Ndipo saona kuwala kwa masana.+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.