29 M’masiku ake, Farao Neko+ mfumu ya Iguputo inabwera kudzathandiza mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate,+ ndipo Mfumu Yosiya inapita kukamenyana ndi mfumu ya Iguputoyo,+ koma mfumuyo inapha Yosiya+ ku Megido+ itangomuona.
20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+