Ezekieli 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ndikadzasandutsa dziko la Iguputo bwinja ndipo zinthu zonse za m’dzikolo zikadzawonongedwa,+ komanso ndikadzapha anthu onse okhala m’dzikolo, anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+ Zefaniya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+
15 “‘Ndikadzasandutsa dziko la Iguputo bwinja ndipo zinthu zonse za m’dzikolo zikadzawonongedwa,+ komanso ndikadzapha anthu onse okhala m’dzikolo, anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+