Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+

  • Ekisodo 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo ndidzalola Farao kuumitsa mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzapezerapo ulemerero mwa kugonjetsa Farao ndi magulu ake onse ankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi momwemo.

  • Salimo 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+

      Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+

      Higayoni.* [Seʹlah.]

  • Ezekieli 30:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ine ndidzabalalitsira Aiguputo ku mitundu ina ya anthu+ ndi kuwamwazira kumayiko ena, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena