Yeremiya 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.
5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.