Numeri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsoka iwe Mowabu! Ndithu mudzafafanizika, inu anthu a Kemosi!+Ndithudi, iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzapereka ana ake aakazi mu ukapolo kwa Sihoni, mfumu ya Aamori. Yesaya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+
29 Tsoka iwe Mowabu! Ndithu mudzafafanizika, inu anthu a Kemosi!+Ndithudi, iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzapereka ana ake aakazi mu ukapolo kwa Sihoni, mfumu ya Aamori.
3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+