Numeri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+ Yoswa 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+ Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa.
30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+
17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa.