Numeri 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni. Amosi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatumiza moto ku Mowabu, ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Kerioti.+ Mowabu adzafa pakati pa phokoso la asilikali, kulira kwa chizindikiro chochenjeza ndiponso lipenga la nyanga ya nkhosa.+
28 Pakuti moto watuluka ku Hesiboni,+ lawi lamoto latuluka m’tauni ya Sihoni.Lanyeketsa Ari+ mzinda wa ku Mowabu, lanyeketsa eni ake a malo okwezeka a ku Arinoni.
2 Ndidzatumiza moto ku Mowabu, ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Kerioti.+ Mowabu adzafa pakati pa phokoso la asilikali, kulira kwa chizindikiro chochenjeza ndiponso lipenga la nyanga ya nkhosa.+