Obadiya 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taonani! Mbadwa za Esau azifufuza paliponse.+ Chuma chake chobisika achifunafuna. Malaki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+
3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+