Yeremiya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ine ndidzawononga zinthu zonse za Esau ndi kumusiya alibiretu kalikonse.+ Ndidzavundukula malo ake obisika+ moti munthu sadzatha kubisala.+ Mbadwa zake, abale ake ndi anthu oyandikana naye adzafunkhidwa,+ ndipo Esau sadzakhalaponso.+
10 Koma ine ndidzawononga zinthu zonse za Esau ndi kumusiya alibiretu kalikonse.+ Ndidzavundukula malo ake obisika+ moti munthu sadzatha kubisala.+ Mbadwa zake, abale ake ndi anthu oyandikana naye adzafunkhidwa,+ ndipo Esau sadzakhalaponso.+