Yeremiya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti unali kuthamanga ndi anthu oyenda pansi ndipo anali kukutopetsa, ndiye ungapikisane bwanji ndi mahatchi?+ Kodi ukumva kukhala wotetezeka m’dziko lamtendere?+ Ndiye udzatani ukadzakhala m’nkhalango zowirira za m’mphepete mwa Yorodano?+
5 Pakuti unali kuthamanga ndi anthu oyenda pansi ndipo anali kukutopetsa, ndiye ungapikisane bwanji ndi mahatchi?+ Kodi ukumva kukhala wotetezeka m’dziko lamtendere?+ Ndiye udzatani ukadzakhala m’nkhalango zowirira za m’mphepete mwa Yorodano?+