11 “Efuraimu anali ng’ombe yaikazi yosaberekapo yophunzitsidwa bwino yokonda kupuntha mbewu,+ ndipo ine ndinapitirira khosi lake lokongola. Koma tsopano ndichititsa wina kukwera pamsana pa Efuraimu.+ Yuda akulima,+ Yakobo akumusalazira zibuma za dothi.+