Yesaya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Monga insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso monga ziweto zopanda wozikusa,+ aliyense wa iwo adzatembenukira kwa anthu ake, ndipo aliyense wa iwo adzathawira kudziko lake.+ Yeremiya 50:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iphani munthu wofesa mbewu mu Babulo,+ ndiponso amene akugwira chikwakwa nthawi yokolola. Aliyense adzabwerera kwa anthu a mtundu wake, ndipo aliyense adzathawira kudziko lakwawo chifukwa choopa lupanga loopsa.+
14 Monga insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso monga ziweto zopanda wozikusa,+ aliyense wa iwo adzatembenukira kwa anthu ake, ndipo aliyense wa iwo adzathawira kudziko lake.+
16 Iphani munthu wofesa mbewu mu Babulo,+ ndiponso amene akugwira chikwakwa nthawi yokolola. Aliyense adzabwerera kwa anthu a mtundu wake, ndipo aliyense adzathawira kudziko lakwawo chifukwa choopa lupanga loopsa.+