Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 45:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndidzakupatsa chuma+ chimene chili mu mdima ndi chuma chobisika chimene chili m’malo achinsinsi, kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, Mulungu wa Isiraeli, amene ndikukuitana ndi dzina lako.+

  • Yeremiya 50:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Lupanga lidzawononga mahatchi awo,+ magaleta awo ankhondo ndi khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana amene ali pakati pawo+ ndipo adzakhala ngati akazi.+ Lupanga lidzawononga chuma chake+ ndipo chidzafunkhidwa.

  • Chivumbulutso 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 katundu yense+ wagolide, siliva, mwala wamtengo wapatali, ndi ngale. Komanso palibe wowagula nsalu zabwino kwambiri, zofiirira, zasilika, zofiira kwambiri, ndi mtengo uliwonse wa fungo lokoma, komanso chilichonse chopangidwa ndi mnyanga, chilichonse chopangidwa ndi mtengo wapamwamba, ndi chamkuwa, chachitsulo, ndi chamwala wa mabo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena