Yeremiya 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 mafumu onse akumpoto, akutali ndi apafupi, mmodzi ndi mmodzi wa iwo, ndipo ndinamwetsanso maufumu ena onse a padziko lapansi. Mfumu ya Sesaki+ nayonso idzamwa pambuyo pa onsewa.
26 mafumu onse akumpoto, akutali ndi apafupi, mmodzi ndi mmodzi wa iwo, ndipo ndinamwetsanso maufumu ena onse a padziko lapansi. Mfumu ya Sesaki+ nayonso idzamwa pambuyo pa onsewa.