Yeremiya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya m’chaka cha 10 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda.+ Chimenechi chinali chaka cha 18 cha Nebukadirezara.+
32 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya m’chaka cha 10 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda.+ Chimenechi chinali chaka cha 18 cha Nebukadirezara.+