6 Iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ukuona zinthu zonyansa kwambiri zimene anthuwa akuchita?+ Ukuona kodi zinthu zimene anthu a nyumba ya Isiraeli akundichitira kunoko kuti nditalikirane ndi malo anga opatulika?+ Koma uonanso zinthu zina zonyansa kwambiri.”