Salimo 78:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+ Yeremiya 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+
60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+
6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+