Hoseya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndinamulembera zinthu zambiri zokhudza malamulo anga,+ koma anangoziona ngati zinthu zachilendo.+ Aroma 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ngati ndiwe Myuda dzina lokha+ ndipo umadalira chilamulo+ ndi kunyadira Mulungu,+
12 Ine ndinamulembera zinthu zambiri zokhudza malamulo anga,+ koma anangoziona ngati zinthu zachilendo.+