Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu wochititsa mantha,+Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+ Salimo 90:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+ Yoweli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzalankhula+ pamaso pa asilikali ake ankhondo+ pakuti anthu a mumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ali ndi mphamvu. Tsiku la Yehova ndi lalikulu+ ndi lochititsa mantha. Ndani angaime pa tsiku limeneli?”+
11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+
11 Yehova adzalankhula+ pamaso pa asilikali ake ankhondo+ pakuti anthu a mumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ali ndi mphamvu. Tsiku la Yehova ndi lalikulu+ ndi lochititsa mantha. Ndani angaime pa tsiku limeneli?”+