Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 38:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndani anagawa ngalande ya madzi osefukira,

      Ndi njira ya mtambo wa mvula yamabingu,+

  • Yesaya 45:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Inu kumwamba, chititsani chilungamo kuvumba ngati mvula.+ Kumwamba kwa mitambo kuchuche chilungamo.+ Dziko lapansi litseguke ndipo libale chipulumutso. Lichititse chilungamo kuphuka+ pa nthawi imodzimodziyo. Ine Yehova ndachititsa zimenezi.”+

  • Yeremiya 51:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo, ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.

  • Zekariya 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula+ pa nthawi ya mvula yomalizira.+ Pemphani Yehova amene anapanga mitambo yamvula+ ndiponso amene amagwetsera anthu mvula yamphamvu.+ Iye amapereka mbewu m’munda mwa munthu aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena