1 Mbiri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kusi anabereka Nimurodi+ amene anali woyamba kukhala wamphamvu padziko lapansi.+