Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+ Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka.
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+
2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka.