Yobu 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+ Yobu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu? Yobu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndinali pa mtendere koma iye anandikhutchumula.+Anandigwira kumbuyo kwa khosi n’kundimenyetsa pansi,Ndipo walunjikitsa mivi yake pa ine. Salimo 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti mivi yanu yandilasa kwambiri,+Ndipo dzanja lanu likundilemera.+
4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+
20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu?
12 Ine ndinali pa mtendere koma iye anandikhutchumula.+Anandigwira kumbuyo kwa khosi n’kundimenyetsa pansi,Ndipo walunjikitsa mivi yake pa ine.