Maliro 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.
2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.